Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Tazunzika kopanda dzuwa
Oh oh oooooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga la ngenewa dululu
Tiyamika mweo apo pamu pando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Tazunzika kopanda dzuwa
Oh oh oooooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga la ngenewa dululu
Tiyamika mweo apo pamu pando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Nakana ku believa ndise tili naminyama
Navenzo mveka bwino vina leka naku wama
Tina lakwila ndani muti kambileko sorry
Mayeso yati konka bad izibika story
First yenze Cholera kwabwela load shedding
Before nama Corona tenze busy nama gassing
Tayambo payana teka teka its so disgusting
Nama busa balema navo va ma fasting
Ku hood kwanga ba guy bafuna che ka certain
Ba vale che pa mala naka nsima ndiye curtain
S'bafuna na vambili umoyo che ni daliso
Ambuye abwezepo nga muchila wa malinso
How did we get here nalema kuzi funsa
Kapena ni udalu sini na silize pa Unza
Agogo anani uza uza kula mwana chipuba
Vika kuvuta langa kumwamba upempe zuba
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Tazunzika kopanda dzuwa
Oh oh oooooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga la ngenewa dululu
Tiyamika mweo apo pamu pando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Nauka mutu uzinguluka monga nenze paka mpewa
Pa fb tayali akali menyana na mwewa
Could it be that im strerssing or making a big fuss
I know that theres somebody looking for a face mask
Coz they die without a proper doctor or a nurse
Without the medication they will end up in a hearse
Are we born with a gift or maybe blessed with a curse
With the after life im certain we might end up in a church
Just not long ago nenzo mvelela seer one
Enze once a topic patu napa bondi panu
Since when chimfine china nkalapo big issue
Sambani ku manja sanitize nama tissue
Now all my shows cancelled im living off my investments
Pray to God he save my family and my bestfriends
Everything quarantined house money car
Pray for zambia for the globe for africa
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Tazunzika kopanda dzuwa
Oh oh oooooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga la ngenewa dululu
Tiyamika mweo apo pamu pando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Tazunzika kopanda dzuwa
Oh oh oooooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga la ngenewa dululu
Tiyamika mweo apo pamu pando
Dzuwa dzuwa dzuwa