Singachitile mwina
Ndabwera ndi chilungamo no lies bola ndikafele zina
Bola ndikafele zina
Sindingachitile mwina
Bola kukathela ku ndende kusiyana ndikumuona ali ndi wina
Iye ali ndi wina
Uyu ndi wanga
Wanga mpaka M'manda
Ngakhale kumwamba
Kwavomeleza
Zoti ndi wanga
Kaya mundimanga
Koma sindikana
Zoti ndi wanga
(ati ndamubela ntima ndikagona mu)
Cello!
Cello!
Cello!
(ati ndamubela ntima ndikagona mu)
Cello!
Cello!
Cello!
(ati ndamubela ntima ndikagona mu)
Ndikagona ku ndende
Mpaka m'mbem'mbe
Kuyesa kulesesa sindingaleke
Kupanga za iweyo mpaka mphete
Babe believe me
Though forever is a long way
Best believe we will get there
I'll love you in the right way mpaka amvesese
Zoti ndi wanga
Wanga mpaka m'manda
Ngakhale kumwamba
Kwavomeleza
Uyu ndi wanga
Kaya mundimanga
Koma sindikana
Zoti ndi wanga
(ati ndamubela ntima ndikagona mu)
Cello!
Cello!
Cello!
(ati ndamubela ntima ndikagona mu)
Cello!
Cello!
Cello!
(ati ndamubela ntima ndikagona mu)