Back to Top

Street Video (MV)




Performed By: Achina Gattah Ase
Language: English
Length: 3:12
Written by: Mike Mkhaya




Achina Gattah Ase - Street Lyrics
Official




Ngati Rapper wako anayimba ndine
Anafa
Ngati Rapper wako sanayimbe ndine
Samatha
Kwama rapper nonse ofuna kuyimba ndine
Simumamva
Osadanda ndikubwela posachedwa
Maranatha
Ndikudzapha mafana a shit
Sindikupola Ili ndi bala lamfana wa sick
Ndinasowa quarantine ndimafana a thick
Ati ma elder ndine
Nigga f*ck that shit
Ine ndi king wa street
Ndapulumutsa game at least
Checka nominations list
Am like oh no please
Gattah newcomer
Mwina chifukwa cha high demand
Judge anakanika kujaja anangowafaka mafana remand
Nanga anakapanga bwanji
Naye amaopa ku blunder
Kumalowa hands nagula cheese crew yanga yonse kubanda
Guardian wa new school mafana makofi akuhanda
Mazifumu mbama ine ndi Gwanda Chakwamba
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Checka nominations list
Am like oh no please
Ine ndi king wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Cheka pama artist list
Oh no rest in peace
Game pakatipa inagona
Musayese ngati mafumu sitimawona
Ma rapper omwe ndinatumiza kunkhondo
Zomvetsa chisoni onse anathela konko
Ofcourse sanadiwe koma anatsala Moscow
Anasiya chamba cha hip-hop anayamba chakonko
Kuyamba kuyimba pakanthawi akuzimva alimomo
Munthu sumakhala legend chifukwa ndiwe mgogo
Mafana amvula zakale
Si size yanga navulaza kale
Kuwaveka khofi kuwavula zakale
Nangowawelenga nkuwachita summary
I took the game back to Btz
I don't give a f*ck about you you're not my real Gz
Kugwila rapper nkhwiko mpaka ngozi
Ndi chifukwa chake ndili Inkosi yamakosi
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Checka nominations list
Am like oh no please
Ine ndi king wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Checka pama artist list
Oh no rest in peace
Ma rapper mu game mwangodzadzana
Dzi beef nde mukudya koma ndidzadzana
Umamva bwanji Gattah akati ndiwe newcomer
Kutenga Spliff kumenya par nkudya Hahahaha
Ana opusa inu eti
Mumawona ngati ine ndi size yanu
[ Correct these Lyrics ]

[ Correct these Lyrics ]

We currently do not have these lyrics. If you would like to submit them, please use the form below.


We currently do not have these lyrics. If you would like to submit them, please use the form below.


English

Ngati Rapper wako anayimba ndine
Anafa
Ngati Rapper wako sanayimbe ndine
Samatha
Kwama rapper nonse ofuna kuyimba ndine
Simumamva
Osadanda ndikubwela posachedwa
Maranatha
Ndikudzapha mafana a shit
Sindikupola Ili ndi bala lamfana wa sick
Ndinasowa quarantine ndimafana a thick
Ati ma elder ndine
Nigga f*ck that shit
Ine ndi king wa street
Ndapulumutsa game at least
Checka nominations list
Am like oh no please
Gattah newcomer
Mwina chifukwa cha high demand
Judge anakanika kujaja anangowafaka mafana remand
Nanga anakapanga bwanji
Naye amaopa ku blunder
Kumalowa hands nagula cheese crew yanga yonse kubanda
Guardian wa new school mafana makofi akuhanda
Mazifumu mbama ine ndi Gwanda Chakwamba
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Checka nominations list
Am like oh no please
Ine ndi king wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Cheka pama artist list
Oh no rest in peace
Game pakatipa inagona
Musayese ngati mafumu sitimawona
Ma rapper omwe ndinatumiza kunkhondo
Zomvetsa chisoni onse anathela konko
Ofcourse sanadiwe koma anatsala Moscow
Anasiya chamba cha hip-hop anayamba chakonko
Kuyamba kuyimba pakanthawi akuzimva alimomo
Munthu sumakhala legend chifukwa ndiwe mgogo
Mafana amvula zakale
Si size yanga navulaza kale
Kuwaveka khofi kuwavula zakale
Nangowawelenga nkuwachita summary
I took the game back to Btz
I don't give a f*ck about you you're not my real Gz
Kugwila rapper nkhwiko mpaka ngozi
Ndi chifukwa chake ndili Inkosi yamakosi
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Checka nominations list
Am like oh no please
Ine ndi king wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ine ndi King wa streets
Ine ndi mfumu ya Gist
Ndapulumutsa game at least
Checka pama artist list
Oh no rest in peace
Ma rapper mu game mwangodzadzana
Dzi beef nde mukudya koma ndidzadzana
Umamva bwanji Gattah akati ndiwe newcomer
Kutenga Spliff kumenya par nkudya Hahahaha
Ana opusa inu eti
Mumawona ngati ine ndi size yanu
[ Correct these Lyrics ]
Writer: Mike Mkhaya
Copyright: Lyrics © O/B/O DistroKid


Tags:
No tags yet